Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #107
Hymn 107 Nthano Ya Yesu Uzeni
[V1]
Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu;
Nthano yodala uzeni, Nthano yoposa zonse.
Nyimbo ya ’ngelo uzeni, Nthawi yobadwa Yesu,
Ulemelero kwa Mlungu, Ndipo mtendere pano.

[C]
Nthano ya Yesu uzeni, Lemba mu mtimangamu,

[V2]
Nena masiku ajawo, Mbuye nasala kudya,
Anayesedwa koopsa, Koma analakika.
Za ntchito yake uzeni, Ndi za zisoni zake,
Anazunzidwa kolimba, Mphawi wopanda kwao.

[V3]
Za mtanda wake uzeni, Ndi za zowawa zake,
Za manda ake uzeni, Ndi za kuuka kwake.
M’nthano ndiona chikondi, Cha Yesu, Mbuye wanga,
Mmene ndiimva ndilira, Anawombola ine.