Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #106
Hymn 106 Tidzamangatu Pa Thanthwe
[V1]
Tidzamangatu pa thanthwelo, Pa thanthwe losatha Yesu,
Tidzaima nji wosagwanso, Pa nthawi ya namondwe.

[C]
Tidzamangatu (tidzamangatu),
Mwa Mbuyathuyo (mwa Mbuyathuyo);
Timanga pa thanthwe lolimbalo, Pa Yesu Khristuyo.

[V2]
Alipo amanga pa mchenga, Pa chuma cha dziko lino;
Ndi ena amanga m’tchimolo, Zokoma za pa dziko.

[V3]
Mangani pa thanthwe Khristuyo, Maziko olimbalimba;
Ndichotu chiyembekezero Cha chip’ulumutso chathu.