Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #79

Hymn 79 Kufuna Antchito

[V1]
Mindatu yayera kale
Dzinthu dzonse dzachanso;
Pafupi ndi kutaliko
M’dziko lonse lapansi.

[C]
Mbuye tikupempha Inu,
Kokosani antchito;
Atumizeni msangatu,
Nthawi isanethe’i.

[V3]
Atumizeni m’mawatu,
Ndi nthawi ya usana;
Ngakhale dzuwa lilowa,
Agwirebe ntchitoyo.

[C]
Mbuye tikupempha Inu,
Kokosani antchito;
Atumizeni msangatu,
Nthawi isanethe’i.

[V4]
Ndipo inu otumidwa,
Gwirani ntchitoyo;
Ndipo potsiriza ntchito
Mudzadza ndi chimwemwe.

[C]
Mbuye tikupempha Inu,
Kokosani antchito;
Atumizeni msangatu,
Nthawi isanethe’i.

79. Kufuna Antchito

Link copied to clipboard successfully!