Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #68
Hymn 68 Ndikonda Kunena Ndaomboledwa
[V1]
Ndikonda kunena chifukwa, Ndaomboledwa ndi mwazi!
Ndaomboledwa mwa chifundo, Ndine wake nthawi zonse.

[C]
Ndi mwazitu (ndi mwazitu) wa Yesu, ndaomboledwa;
Ndine wake (ndine wake) kosatha, ndaomboledwa.

[V2]
Ndinetu wokondwa mwa Yesu, Kukondwa kosaneneka;
Ndziwa kuti kuwala kwake Kumakhalabe ndi ine.

[V3]
Ndisinkha za Mombolo wanga, Tsiku lonse ndisinkha ’Ye,
Ndiyimba wosakhala chete, Ndiyimba chikondi chake.

[V4]
Ndidziwa kuti ndzamuona, Mfumu amene ndimkonda;
Yemwe amanditsogolera, Ndi kundisunga usiku.

[V5]
Korona ali kudikira, Mmalo anga owalawo;
Msanga ndi oyera mtimawo Ndidzakhala ndi Ambuye.