Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #16

Hymn 16 Timapazi Inu, Samalirani

[V1]
I WASHED MY HANDS1. Ndasamba m’manja mwanga, Mwayeretsedwatu,
Ndi kwapereka iwo, Ku ntchito ya Yesu.

[C]

Timapazi inu Samalirani,
Musanditengere, Kuli zoipa.

[V2]
Makutu amvetsere Pa tsiku lonseli,
Ntchito yonse yabwino, Manjawa achite.

[C]

Timapazi inu Samalirani,
Musanditengere, Kuli zoipa.

[V3]
Maso anga aone, Ntchito zawo zonse,
Kutitu asachimwe, Chifukwa cha Yesu.

[C]

Timapazi inu Samalirani,
Musanditengere, Kuli zoipa.

16. Timapazi Inu, Samalirani

Link copied to clipboard successfully!