Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #60
Hymn 60 Yesu Chimwemwe Chathu
[V1]
Yesu chimwemwe chathucho, Chitsime ndinu cha moyo.
Ku’nika kwa ’nthu onsewo, Tibwera kwanu Mbuyathu.

[V2]
Polawa mkate wa moyo Tilakalaka kudyanso.
Pakumwa madzi a moyo Tikwanitsidwa ndi Inu.

[V3]
Mtima ufuna Inuyo Kumene mtitumizako
Tidzakondwera ngatitu Tigwira Inu kolimba.

[V4]
Yesu, mukhale nafetu; Musangalatse ifenso.
Muchotse mdima wa tchimo, Muwale mdziko lonseli.