Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #58

Hymn 58 Mumbveke Mbuyeyo

[V1]
Tamani mphamvu ya Yesu angelo agwade;
Tulutsanitu korona mumveke Mbuyeyo
Tulutsanitu korona mumveko Mbuyeyo.

[V2]
Inu osankhidwa ake, Owomboledwa’nu,
Tamani Mpulumutsiyo, mumveke Mbuyeyo;
Tamani Mpulumutsiyo mumveko Mbuyeyo.

[V3]
Anthu onse ndi mitundu, Pa dziko linotu,
Am’lemekeze Mfumuyo, mumveke Mbuyeyo;
Am’lemekeze Mfumuyo, mumveke Mbuyeyo.

[V4]
Tifuna kuti komweko, Tikamgwadire’Ye
Tidzayimba kosaleka mumveke Mbuyeyo
Tidzayimba kosaleka mumveke Mbuyeyo.

58. Mumbveke Mbuyeyo

Link copied to clipboard successfully!