Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #54

Hymn 54 Ndifuna Inu, Mbuyanga

[V1]
Ndifuna Inu, Mbuyanga, Chifukwa ndagwa mthopemo,
Ndi madzi pena motowo, M’nditsuke ’ne, mnditsuke ’ne.

[C]
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Achoketu mu mtimanga.

[V2]
Mukatsegula masowa, Ndidzakuyamikani ’Nu.
Komabe Mtima woyera, Udzapambana zonsezo.

[C]
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Achoketu mu mtimanga.

[V3]
Ukatsukidwa mtimawo Adzatseguka masowo.
Chifukwa kuti mwa Inu, Ndionamo za mmwambamo.

[C]
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Achoketu mu mtimanga.

[V4]
Ndayesa kudzikonzatu, Kuchotsa tchimo langalo
Ngakhale ndayesetsatu, Zoipazo zilipobe.

[C]
Mnditsuke ’ne mu mtimamo, Ndi madzi pena motowo.
Mnditsuke ’ne machimowo, Achoketu mu mtimanga.

54. Ndifuna Inu, Mbuyanga

Link copied to clipboard successfully!