Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #55

Hymn 55 Kodi Mwalandira Yesu?

[V1]
Kodi mwalandira Yesu Mbuyeyo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?
Mwakhulupirira mwa chisomo ’ke?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[C]
Kodi mwasambamo,
Mmwazi wabwino wa Yesuyo?
Kodi mwayeretsa mtima wanuwo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[V2]
Kodi mukuyenda ndi Ambuyeyo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?
Mwapumula mwa Wopachikidwayo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[C]
Kodi mwasambamo,
Mmwazi wabwino wa Yesuyo?
Kodi mwayeretsa mtima wanuwo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[V3]
Kodi mwakonzeka pa kubwera ’Ye?
Kodi mwasamba mmwazi wake?
Kuti mukalowe m’malo abwino,
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[C]
Kodi mwasambamo,
Mmwazi wabwino wa Yesuyo?
Kodi mwayeretsa mtima wanuwo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[V4]
Tayanitu zakunyansa zanuzo,
Kodi mwasamba mmwazi wake?
Wakuchotsa tchimo lanu lonselo,
Kodi mwasamba mmwazi wake?

[C]
Kodi mwasambamo,
Mmwazi wabwino wa Yesuyo?
Kodi mwayeretsa mtima wanuwo?
Kodi mwasamba mmwazi wake?

55. Kodi Mwalandira Yesu?

Link copied to clipboard successfully!