Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #125

Hymn 125 Muli Dzuwa M’phiri Muja

[V1]
Muli dzuwa m’phiri muja, Muli dzuwa m’nyanjamo;
K’wala kwake kumagwera Pa maudzu ponsepo;
Koma dzuwa lopambana Lili m’mtima mwangamu;
Ka’mba komwe mukhalitsa, Kuli dzuwa lowala.

[C]
Muli dzuwa lakuwalitsa! Muli dzuwa m’mtimanga.
Yesu adzachotsa mdima, Muli dzuwa m’mtimanga.

[V2]
Ndisiya ’ne nsoni zanga Ndi zovala za nsanza;
Mundivekatu zoyera, Ndiyamika m’mtimamo;
Kuli malo a ulemu Munandikonzera ’ne;
Mtima wanga ufunako, Ndidzatsata Inutu.

[C]
Muli dzuwa lakuwalitsa! Muli dzuwa m’mtimanga.
Yesu adzachotsa mdima, Muli dzuwa m’mtimanga.

[V3]
Inu, Yesu, mwandigula, Ndine wanu konseko,
Munayatsa nyali yanga, Iwalire Inuyo;
Kuli malo a ulemu Munandikonzera ’ne,
Mtima wanga ufunako, Ndidzatsata Inuyo.

[C]
Muli dzuwa lakuwalitsa! Muli dzuwa m’mtimanga.
Yesu adzachotsa mdima, Muli dzuwa m’mtimanga.

125. Muli Dzuwa M’phiri Muja

Link copied to clipboard successfully!