Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #30
Hymn 30 Dzuwa Lili Kulowa
[V1]
DAY IS DYING IN THE WEST 1. Dzuwa lili kulowa, Mlungu atipumitse;
Linda ndi kupemphera mmene nyali zili kuwala m’mwamba.
DAY IS DYING IN THE WEST 1. Dzuwa lili kulowa, Mlungu atipumitse;
Linda ndi kupemphera mmene nyali zili kuwala m’mwamba.
[C]
Woyera Ambuye wa makamu!
Za m’mwamba ndi za dziko zitamanda Inu,
Mlungu Wamkulu.
Woyera Ambuye wa makamu!
Za m’mwamba ndi za dziko zitamanda Inu,
Mlungu Wamkulu.
[V2]
Ambuye wamoyo’Nu, Ife tasonkhanatu,
Kufuna nkhope Yanu; mutifungatire’fe m’khola Lanu

[V3]
Pamene mthunzi ugwa, Mumatifungatira;
Mwa chisomo chanutu, Mitima yathu ikwera kwa Inu.

[V4]
Tikamwalira ife osaona za dziko,
Ambuye wachifundo, mutidzutsenso tsiku lotsiriza.