Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #14

Hymn 14 Imva Makobidi

[V1]
HEAR THE PENNIES DROPPING1. Imva makobidi, tili kuponya!
Tili kupereka, onse kwa Yesu.

[C]

Ngwingwi! ngwingwi! Ngwingwi! ngwingwi!
Tili kuponya! Tili kupereka, Onse kwa Yesu.

[V2]
Tonse tipereka, kobidi lathu;
Kuti anthu ena amve za Yesu.

[C]

Ngwingwi! ngwingwi! Ngwingwi! ngwingwi!
Tili kuponya! Tili kupereka, Onse kwa Yesu.

[V3]
Pakuperekatu tili kusunga;
Tikakula, Mbuye adzatipatsa.

[C]

Ngwingwi! ngwingwi! Ngwingwi! ngwingwi!
Tili kuponya! Tili kupereka, Onse kwa Yesu.

[V4]
Makamaka Yesu afuna ife;
Kuti tipereke mitima yathu.

[C]

Ngwingwi! ngwingwi! Ngwingwi! ngwingwi!
Tili kuponya! Tili kupereka, Onse kwa Yesu.

14. Imva Makobidi

Link copied to clipboard successfully!