Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #335
Hymn 335 Pofunafuna M’malembo Ace
[V1]
SEARCHING THE SCRIPTURES 1. Pofunafuna m’malembo ace, Pofuna Mpulumutsiyo,
Momwe tikumva za Ambuye, Bible amati c’ani ko?

[C]
Pita, kafunse, ati Mfumu, Ka’mba ka iwe, ndinetu
Pita, gogoda khomo lace, Komwe udzapumulako.
2. Pofunafuna m’malembo ace, Tiri kufuna njirayo
Yonka ku mzinda wopambana, Bible amati c’ani ko?
3. Pofunafuna m’malembo ace, Pofuna otaikawo,
Kuwatsogoza kwa Ambuye, Bible amati c’ani ko?