Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #336
Hymn 336 Usikuwo Woyerawo
[V1]
SILENT NIGHT 1. Usikuwo woyerawo, Mwana adamlerayo,
Akakhale Mfumuyo, Anabadwa m’kholamo
Mfumu ya Mafumu, Ndi ya anthuwo.
2. Mwanayo wa Mulunguyo, Andikonda inetu,
Nantayira cumaco, Nadzagona M’udzumo,
Ndiyamika Mbuye Wanga Yesuyo
3. Usikuwo woyerawo, Nudzatu Mtenderewo,
Ife tonse anthuwo, Atitenga Mlunguyo;
Mlemekeze "Tate, Mwana, Mzimunso.