Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #334
Hymn 334 Mmene Ine Ndisauka
[V1]
WHEN THE STORMS OF LIFE 1. Mnene ine ndisauka Ndi zoipa zangazo
Ndidzapita kwa Mulungu, Adzandilandiratu

[C]
Mlungu adzalandira, Iye ndiye Atate wanga,
Watumiza Mwana wace, Anandifera kalelo.
2. Ngati atsamwali anga sandikonda ine bi.
Ndikhulupirire Mlungu, Iye sandikanai.
3. Pansi pano ndiri mlendo, Kwathu ndi kumwambako,
Mmene adzabwera Yesu Ndidzapita komweko.