Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #333
Hymn 333 Tikagwidwa Ndi Cisoni
[V1]
WE ARE SORROWFUL 1. Tikagwidwa ndi cisoni, Ikayendanso misozi,
Poliriratu abale, Yesu mutimveretu.
2. Munabvala thupi lathu, Munadziwa masauko
Mnalirira bwenzi lanu, Yesu mutimveretu.
3. Mmene imfa yathu idza, Mwenya wathu ukaleka
Mmene ife timwalira, Yesu mutiveretu.
4. Mnamwalira Inu paja, Mwazi wanu munataya,
Inu munagona m’manda, Yesu mutimveretu.