Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #332
Hymn 332 Pakukhala Pa Mgonero
[V1]
WHILE IN SWEET COMMUNION 1. Pakukhala pa mgonero, Wa Ambuye wathuyo,
Tionetu mwazi wanu, Muja unakheramu
Nkana singaone Inu, Muli mfupi nafedi,
Mutsangalatse, Mbuye
2. Mutiuze ife nthano Ya mabvuto anuwo,
Pakuyembekeza Inu, Tisendeza kwanuko
Mtikokere mfupi ndi ’Nu, Ndi ku mtanda wanuwo,
Mpaka tidzaone tokha, Monga munaona ’fe.
3. Pakucoka pa mgonero, Wa Ambuye wathuyo,
Moyo wathu ufanane, Ndi wa Mbuye wathuyo,
Pakutsanza moyo wace, Tisanduka Iyeyo.
Timuchula wathu, Pakumvera mau ’ce.