Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #318
Hymn 318 Tsiku La Sabata
[V1]
HOLY SABBATH DAY 1. Tsiku la Sabatalo, Mlungu nalipatula;
Atalenga zonsezo, Mbuye napumulanso.
HOLY SABBATH DAY 1. Tsiku la Sabatalo, Mlungu nalipatula;
Atalenga zonsezo, Mbuye napumulanso.
[C]
Tsiku la Sabatalo, Mlungu nalidalitsa;
Kukumbutsa ife za mphamvu ya kulengayo.
2. Musafune za dziko, Ndi zokondweretsa
Kuli zopambanadi M’dziko la kumwambako.
3. Pakuyamba tsikulo, Loweruka madzulo
Tisonkhane tonsefe, Kuyimbira Mbuyeyo.
4. Tipemphere nsisizo, Ndi gonjetso lacelo,
Kuti athangate, ’fe Kulisunga tsikulo.
Tsiku la Sabatalo, Mlungu nalidalitsa;
Kukumbutsa ife za mphamvu ya kulengayo.
2. Musafune za dziko, Ndi zokondweretsa
Kuli zopambanadi M’dziko la kumwambako.
3. Pakuyamba tsikulo, Loweruka madzulo
Tisonkhane tonsefe, Kuyimbira Mbuyeyo.
4. Tipemphere nsisizo, Ndi gonjetso lacelo,
Kuti athangate, ’fe Kulisunga tsikulo.