Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #319
Hymn 319 Ndidzayimba Za Mulungu
[V1]
I WILL SING 1. Ndidzayimba za Mulungu Za Kukonda kwaceko
Watumiza mwana wavce, Kundifera kalelo

[C]
Inde ndidzayimba nyimbo, Ya kukonda kwaceko,
Ndidzayimba ndi angelo, Akukhala m’mwambamo.
(Bass, Alto, and Tenor):
Yimbatu, ndiyimba nyimbo; Kondako, kondako, yimbatu;
Angelo omwe, Akukala m’mwambamo, E, M’mwambamo.
2. Ndinacita mphulupulu, Waiwala zonsezo,
Ndinakhala ndi zoipa, Wazicotsa zonsezo
3. Wandipatsa moyo wace, Moyo wakuyera mbu,
Ine ndiri mwana wace, Wandilera inetu.
4. Ndiyamika Mbuye wanga, Ndidzamlemekezatu,
Ndipititsa mbiri yace, Ya kukonda kwaceku.