Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #282
Hymn 282 Mingoli Zikwi Khumi
[V1]
TEN THOUSAND HARPS 1. Ha! Mingoli ndi maunso Alemekeza m’mwamba;
Yesu m’mwambamo akondwa; Alamula ponsepo;
Ali pa mpando uko; Yesu alamulira
Aliluya! Aliluya! Aliluya! Amen
2. Krona wanu sabvulidwa, Mfumu yolemerera;
Cikondi canu cosatha, Kwa anthu onse;
Anthu anu okondwa Adzaona nkhopeyo
Aliluya! Aliluya! Aliluya! Amen.
3. Ambuye idzani msanga tsikulo tilisowa
Kudzamvetsera tsikulo, m’mwamba ndi dziko zatha’
Tidzaliza mingoli Ulemu kwa Mfumuyo.