Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #262

Hymn 262 Kristuu Kapena Barab

[V1]
CHRIST OR BARABAS 1. Nditani naye Yesu? Waima panoyu
Wabvala cinyong’onyo, Ndi minga pamutu.

[C]

Tsopano ndifunse, Muyankha cotani?
Ndimpacike Mfumu Yesu, Atsale Baraba?

2. Ndimasule mbalayi, Cimunthu ca dama?
Wocimwa, ngosacimwa? Mukanapo yani?

3. Funsotu loopsali! Litengeni bwino,
Nsisi zilindirabe, Koma mwa mabvuto.

4. Mpando waciweruzo sungakane dziko?
Anapfuula "Cotsa, Mumpacike Yesu!"

5. Si kwa ocimwa okha Funso linenetse;
Mvani Akristu nomwe, Ora loyesedwa

262. Kristuu Kapena Barab

Link copied to clipboard successfully!