Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #247
Hymn 247 Angelo Ayimba Kumwamba
[V1]
SING THE BELLS OF HEAVEN 1. Mabelo kumwamba! Kuli cimwemwe,
Akatembenuka wocimwa;
Tate amucingamira kunjira,
Mwana wotopa wosocera.
SING THE BELLS OF HEAVEN 1. Mabelo kumwamba! Kuli cimwemwe,
Akatembenuka wocimwa;
Tate amucingamira kunjira,
Mwana wotopa wosocera.
[C]
Angelo ayimba kumwamba;
Ulemu, ulemu m’mingoli,
Opulumukawo abvekedwa mbu,
Ayimbira molemekeza.
2. Mabelo kumwamba! Kuli cimwe
Wotayika wabvomeredwa;
Wocimwayo wabwezedwa ku chimo,
Wabadwanso ngati walero.
Angelo ayimba kumwamba;
Ulemu, ulemu m’mingoli,
Opulumukawo abvekedwa mbu,
Ayimbira molemekeza.
2. Mabelo kumwamba! Kuli cimwe
Wotayika wabvomeredwa;
Wocimwayo wabwezedwa ku chimo,
Wabadwanso ngati walero.