Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #246
Hymn 246 Mnenere Yesu Liu
[V1]
JUST A WORD FOR JESUS 1. Mnenere Yesu liu; Bwenzi la pamtima,
Utiuzetu zomwe; Anakucitira.
JUST A WORD FOR JESUS 1. Mnenere Yesu liu; Bwenzi la pamtima,
Utiuzetu zomwe; Anakucitira.
[C]
Pomunenera Yesu Zidzatithandiza;
Mau pang’ono pokha, Nenga, yimba, pempha.
2. Mnenere Yesu liu; Wakhululukidwa,
Ndi kuyesayesako, Ufike kumwamba.
3. Mnenere Yesu liu, Kukana sinditha;
Ndikonda Mpulumutsi, Wondiombolayo.
4. Mnenere Yesu liu, Usataye nthawi;
Wozemba ntchito yace, Apeza cisoni.
5. Mnenere Yesu, liu, Pocepa nkhongono;
Dzuka ukafooka, Mlekere zinazo.
Pomunenera Yesu Zidzatithandiza;
Mau pang’ono pokha, Nenga, yimba, pempha.
2. Mnenere Yesu liu; Wakhululukidwa,
Ndi kuyesayesako, Ufike kumwamba.
3. Mnenere Yesu liu, Kukana sinditha;
Ndikonda Mpulumutsi, Wondiombolayo.
4. Mnenere Yesu liu, Usataye nthawi;
Wozemba ntchito yace, Apeza cisoni.
5. Mnenere Yesu, liu, Pocepa nkhongono;
Dzuka ukafooka, Mlekere zinazo.