Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #245
Hymn 245 Palibe Dzina Lina
[V1]
NO OTHER NAME 1. Dzina lokhalo la Yesu, Ndilo dzina lokoma;
Likondwetsa ’ngelo m’mwamba, Ndi Akhristu tonsefe.

[C]
Dzina, dzina, Palibe longa la Yesu,
Dzina, dzina, Palibe longa la Yesu.
2. Dzina lokha ndi la Yesu, Pamene ndibvutika;
Dzina lokha ndi la Yesu pamene ndikondwera.
3. Ndikufuna kudzamwona, Podza mu’lemerero,
Ndidzamve Wacita bwino, Ndidzakondwererako.
4. Ngat’ afuna ngwire ntchito, M’munda wace wa mpesa,
Kuli bwino Yesu yekha, ’Dalitse ntchito zanga.
5. Ngat’afuna kuti ndife, Akhudze thupi langa,
Kukhale bwino ndi Yesu, Ndikhulupira mwa’ye.