Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #243
Hymn 243 Dzuwa Moyowe
[V1]
ARISE MY SOUL, ARISE 1. Dzuka moyo wanga, Cotsa mantha ako;
Nsembe ya mwaziwo, Cifukwa ca ine;
Indiimira ku mpando, Indiimira ku mpando;
Dzina langa lalembedwa.
2. Kumwamba alipo, Kundipembedzera,
Cikondi caceco, Cinakhetsa mwazi;
Anatifera tonsefe, Anatiferea tonsefe,
Awaza mpando wansisi.
3. Mabala asanu, Anapwetekapo;
Mutu "khululukani" Atitu "khululukani,"
Msalole wolapa afe!
4. Tate amamumva, Wodzozedwa wace;
Sangacotse mwana, Wofika kwa Iye,
Mzimu ubvomera mwazi, Mzimu ubvomera mwazi,
Ndabadwira mwa mulungu.
ARISE MY SOUL, ARISE 1. Dzuka moyo wanga, Cotsa mantha ako;
Nsembe ya mwaziwo, Cifukwa ca ine;
Indiimira ku mpando, Indiimira ku mpando;
Dzina langa lalembedwa.
2. Kumwamba alipo, Kundipembedzera,
Cikondi caceco, Cinakhetsa mwazi;
Anatifera tonsefe, Anatiferea tonsefe,
Awaza mpando wansisi.
3. Mabala asanu, Anapwetekapo;
Mutu "khululukani" Atitu "khululukani,"
Msalole wolapa afe!
4. Tate amamumva, Wodzozedwa wace;
Sangacotse mwana, Wofika kwa Iye,
Mzimu ubvomera mwazi, Mzimu ubvomera mwazi,
Ndabadwira mwa mulungu.