Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #222

Hymn 222 M’manja A Yesu Wanga

[V1]
SAFE IN THE ARMS OF JESUS 1. M’manja a Yesu wanga ndiri kugonamo,
Mommo aphimba ine naco cikondico.
Mvera! Mudzera mmwamba mau a Yesu wanga,
"Mwana ndisungira pano pa matima panga"

[C]

M’manja a Yesu wanga ndiri kugonamo,
Mommo aphimmba ine naco cikondico.

2. M’manja a Yesu wanga nkhawa zonsezi zi!
Momwe zoipa zanga sizindibvuta bi.
Mommo mulibe nsoni, mommo mokoma monse.
Sindiliramo msozi, nkondwa ndi Mtima wonse.

3. Mtima umabisala m’manja mwa Yesumo,
Mbuye musunge ine, ndikhulupira ’Nu.
Mommo wa cete ine mpaka wocoka mdima,
Tsono ndiona komwe Yesu wokoma Mtima.

222. M’manja A Yesu Wanga

Link copied to clipboard successfully!