Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #160

Hymn 160 Yesu Andisungetu!

[V1]
Yesu andisungetu!
Ndi mphamvu yakeyo;
Dziko lisandidetse;
Kuti nditsate ’Ye.

[C]
Yesu andisungetu!
Mbuye ndipempha ’Nu;
Inetu ndine chabe, chabe,
Inu ndi zonsezo.

[V2]
Yesu andisungetu!
Nditumikire ’Ye;
Ndichitetu kufuna,
Kwa Yesu, Mbuyeyo.

[C]
Yesu andisungetu!
Mbuye ndipempha ’Nu;
Inetu ndine chabe, chabe,
Inu ndi zonsezo.

[V3]
Yesu andisungetu!
Dziko ndilisiya;
Ndikhaletu wofatsa,
Woyera mtimamo.

[C]
Yesu andisungetu!
Mbuye ndipempha ’Nu;
Inetu ndine chabe, chabe,
Inu ndi zonsezo.

[V4]
Yesu andisungetu!
N’khaletu wakeyo;
N’khaletu wake yekha,
Ku nthawi zonsezo.

[C]
Yesu andisungetu!
Mbuye ndipempha ’Nu;
Inetu ndine chabe, chabe,
Inu ndi zonsezo.

160. Yesu Andisungetu!

Link copied to clipboard successfully!