Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #149

Hymn 149 Yenda Mkuunika

[V1]
Yenda mk’unika kwakeko, Atsogolere ’we;
Ndi Mzimu wa kumwambayo ’Dzainga mdimawo.

[C]
Yendanibe, Mkuunikatu;
Yendanibe, Mkun’ikatu kwa Mlunguyo.

[V1]
(Bass and Tenor):
Yendanibe mku’nikatu kwa Mlunguyo,
Yendanibe mku’nikatu kwa Mlunguyo,
Yendanibe mku’nikatu kwa Mlunguyo;
Mku’nikatu kwa Mlunguyo.

[C]
Yendanibe, Mkuunikatu;
Yendanibe, Mkun’ikatu kwa Mlunguyo.

[V2]
Yenda mku’nika Yesuyo, Wowala m’mauyo,
Atsogolera onsewo, Okhulupirawo

[C]
Yendanibe, Mkuunikatu;
Yendanibe, Mkun’ikatu kwa Mlunguyo.

[V3]
Nkana mithunzi igwetu, Kudetsa njirayo.
Mdimawo udzathawatu, Ku’nika kwakeko.

[C]
Yendanibe, Mkuunikatu;
Yendanibe, Mkun’ikatu kwa Mlunguyo.

[V4]
Yenda mku’nika kwakeko, Udziwe nsisizo,
Chikondi chidzaposadi, Pofika mmwambamo.

[C]
Yendanibe, Mkuunikatu;
Yendanibe, Mkun’ikatu kwa Mlunguyo.

149. Yenda Mkuunika

Link copied to clipboard successfully!