Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #141

Hymn 141 Ndikhaletu Wanu

[V1]
Ndikhaletu wanu, Mbuyanga; Konseko, konseko,
E, kufuna kwanu ndichite, Mndithandizetu.

[C]
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu, Mbuyanga;
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu leroli.

[V2]
Chuma ninji ko popandatu Inuyo, Mbuyanga,
Ndidzasiya zinthu zonsezo, Ndidzatsata ’Nu.

[C]
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu, Mbuyanga;
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu leroli.

[V3]
Pofulatira ’ne dzikoli, Mkhaletu nanenso;
Inu ndinu Chuma changacho; Mnditonthozetu.

[C]
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu, Mbuyanga;
Wanutu (Mbuye), wanutu (Mbuye), Ndine wanu leroli.

141. Ndikhaletu Wanu

Link copied to clipboard successfully!