Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #110
Hymn 110 Odala Ali Akuchita
[V1]
Imva mau a Mpulumutsi,
Mau owona a moyo;
Wosasamalawe kumbukiratu,
Odala ali akuchita.
Imva mau a Mpulumutsi,
Mau owona a moyo;
Wosasamalawe kumbukiratu,
Odala ali akuchita.
[C]
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.
[V2]
Ngakhale timve malamulo,
Ndi malonjezano ake;
Kumvako sikungatipulumutse,
Odala ali akuchita.
Ngakhale timve malamulo,
Ndi malonjezano ake;
Kumvako sikungatipulumutse,
Odala ali akuchita.
[C]
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.
[V3]
Adzalowa mu mzinda uja,
Opanda tchimo ndi imfa;
Atayeretsedwa kwa nthawi zonse,
Adzadya za mtengo wa moyo.
Adzalowa mu mzinda uja,
Opanda tchimo ndi imfa;
Atayeretsedwa kwa nthawi zonse,
Adzadya za mtengo wa moyo.
[C]
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.
Odala ochita malamulo,
Odalatu odalatu;
Odala ochita malamulo,
Odala ndi akuchita.