Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #1
Hymn 1 Omba Lipenga
[V1]
WATCHMAN, BLOW THE GOSPEL TRUMPET1 Mlonda lalika uthenga, Chenjeza anthu onse,
Iye wakumva adzetu, Nakhale nawo moyo.

[C]
Omba Lipenga mlonda’we, Anthu onse amvetu,
Lalika atero Mlungu! Onse amasulidwe.

[V2]
Lalika m’mapiri monse, M’nkhalango ndi m’madambo;
Lalikiranso mzinyanja, Ndi nyimbo yokondwera.

[V3]
Lalikira ponse ponse, kumene kuli mdima;
Amve kuti zonse zapsa, Atate alindira.

[V4]
Lalikira kwa othodwa, Akufuna mpumulo;
Yesu ali kuitana, Idzani kwa inetu.