Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #302

Hymn 302 Mulungu Wa Kumwamba

[V1]
(Upon Dedicating a Church) 1. Mulungu wa kumwamba, tabwera kunoku,
Ndi Mtima wokondwera kulowa m’nyumbayi
Cifukwa ca zabwino mwacitazi
Titokuyamikirani leroli.

[C]

Inde tikuyamikani, Atate, leroli,
Mwatimangira ’fe kuno kacisi wanuyu!
Ndi ulemerero wanu mudzadze m’mnyumbayi;
Muyeretse, mudalitse, munomu

2. Tikondwa tonse kukuthokozani ’Nu
Poyamba kupemphera ndi kuyimbiramu
Mom’muno nsiku zonse mukhale nafetu
Monga nd angelo anu m’mwambamo.

3. Ikhale ngati nyali, yowala m’nyumbayi,
Yakutsogoza onse opunthwa m’mdima bii,
Akunja ndi Akhristu mwapulumutse ndi kuunika koturuka munomu.

302. Mulungu Wa Kumwamba

Link copied to clipboard successfully!