Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #301

Hymn 301 Ambuye Ali Pafupi Kudza

[V1]
’TIS ALOMOST TIME FOR THE LORD TO COME 1. Ambuye ali pafupi kudza, Ndikumvaconcodi,
Ndiponso nyenyezi zikuzima, Tsopano ndi mbanda kucatu

[C]

Ee! Tsopano ndi mbanda kucatu!
Ee! Tsopano ndi mbanda kuca ndithu!
Usiku wathadi! Usana wadzanso.
Ee! Tsopano ndi mbanda kucatu!

2. Zizindikiro za mlengalenga Zilalikiradi;
Ndi za pa dziko zinena kuti Ambuye wayandikira

3. Ndi nthawi yoti kunyada kuthu Mu mpingo wonsewo;
Ukhale wofulumira ntchito, Ukhale woyang’aniratu

4. Pitani msanga kukalalika Kwa osaukawo;
Ndi kwa omveka a dziko lino; Onsewo afulumirenso.

301. Ambuye Ali Pafupi Kudza

Link copied to clipboard successfully!