Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #299

Hymn 299 Tikondwere Nthawi Zonse

[V1]
ALWAYS CHEERFUL 1. Tikondwere nthawi zonse; Tidandauliranji
Kwina "Tate wathu Mlungu, Atisamalirafe?

[C]

Tikondwere nthawi zonse Ponse dzuwa liwala
Njira ya ntchitoyi ndi yokoma
Tikondwere konseko.

2. Dzanja lace litsogoza, Ngati chimo lidzatu
Nsisi zace, Satisiya tokha bi.

3. Tikaleka ntchito yathu, Tidzacita macimo,
Ndipo mtambo wa cisoni, Udzaletsa cimwemwe.

4. Abwinowo akondwere, Ndi mtendere wosatha
Timveretu mau ace, Tikonde zokomazo.

299. Tikondwere Nthawi Zonse

Link copied to clipboard successfully!