Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #284

Hymn 284 Popita Masikuwa

[V1]
WHILE THE DAYS ARE GOING BY 1. Kuli anthu obvutika, Popita masikuwa,
Kuli anthu akutopa, Popita masikuwa;
Ngati tiwakondwetsa, Poyenda ulendowu
Zabwino ticitetu, Popita masikuwa.

[C]

Masiku apita, Masiku apita,
Zabwino ticitetu! Popita masikuwa.

2. Kulibe nthawi yotaya, Popita masikuwa;
Mukhale osangalala, Popita masikuwa;
Dziko liri m’cisoni, Misozi ndi maliro;
Thandiza obvutika, Popita masikuwa.

3. Zotimanga tizisiya, Popita masikuwa;
Modzi ndi mmodzi atsala, Popita masikuwa
Zabwino tidzakhala, ponse ponse zimera;
Tidzakhala okondwa, Popita masikuwa.

284. Popita Masikuwa

Link copied to clipboard successfully!