Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #265
Hymn 265 Mtenderewo
[V1]
PEACE, PERFECT PEACE 1. Mtenderewo, m’dziko la mdimali;
Mwazi wa Yesu unong’oneza.
2. Mtenderewo, m’ntchito zocuruka;
Ntchito ya Yesu ndiko kupuma.
3. Mtenderewo, m’bvuto lotizinga;
Mtendere uli mwa Yesu yekha.
4. Mtenderewo, anga ali m’tari
Yesu asunga ine ndi iwo.
5. Mtenderewo, uli m’tsogolomo;
Tidziwa Yesu ali pa mpando.
PEACE, PERFECT PEACE 1. Mtenderewo, m’dziko la mdimali;
Mwazi wa Yesu unong’oneza.
2. Mtenderewo, m’ntchito zocuruka;
Ntchito ya Yesu ndiko kupuma.
3. Mtenderewo, m’bvuto lotizinga;
Mtendere uli mwa Yesu yekha.
4. Mtenderewo, anga ali m’tari
Yesu asunga ine ndi iwo.
5. Mtenderewo, uli m’tsogolomo;
Tidziwa Yesu ali pa mpando.