Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #250

Hymn 250 Chimo Musalole

[V1]
YIELD NOT TO TEMPTATION 1. Chimo musalole, Limacimwitsa,
Gonjetso limodzi Libweza wina;
Pitani m’tsogolo, Zoipa leka,
Yang’ana kwa Yesu, Adzakusunga.

[C]

Funsa Mbuye thandizo
Aszakusunga iwe;
Ali wolola Iye;
Adzasunga iwe.

2. Thawani oipa, Ndi otukwana,
Lemekeza Mlungu, Osamamnyoza;
Khala waulemu, Ndi wacifuno,
Yang’ana kwa Yesu, Adzakusunga.

3. Kwa wolakikayo, Korona ’patsa,
Mwa cigonjetsoco, Kwa opirira;
Mpulumutsi wathu, Adzalimbitsa,
Yang’ana kwa Yesu, Adzakusunga.

250. Chimo Musalole

Link copied to clipboard successfully!