Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #241
Hymn 241 Dziko Labwino
[V1]
BEULAH LAND 1. Ndapeza dziko lokoma, Ndi zinthu zonse ndi zanga;
Zokometsetsa konseko, Usiku wandicokera.

[C]
O, dzikolo, lokomalo, Pa phiri lokometsalo,
Ndipenyetsetsa ku Nyanja, Manyumba andikonzera,
Ndiyang’anitsa dzikolo, Komwe ndidzakhalitsako.
2. Ndiyenda ndi Mpulumutsi, Andikondwera m’njiramo;
Anditsogolera bwino, Kumwamba ndikafikeko.
3. Mphepo zinunkhira bwino, Za mitengo ya dzikolo,
Maluwa nao safota, Mitsinje simaumako.
4. Mphepo za kumadzulozo, Ndi nyimbo kumwambako,
Angelo onyezimira Ayimba za mphamvu zace.