Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #213
Hymn 213 Nyimbo Yanga
[V1]
MY SONG 1. Yesu mombolo wanga, Ndinu nyimbo yanga
Mpulumutsi wabwino, Ndikamabvutika
MY SONG 1. Yesu mombolo wanga, Ndinu nyimbo yanga
Mpulumutsi wabwino, Ndikamabvutika
[C]
Yesu Mombolo wanga, Ndiyimbira Inu;
Palibe bwenzi lina, Ndikondana nalo.
2. Ndiyembekezera’nu, Mwa zaka zonsezi,
Ndikapanikizidwa, Polira misozi.
3. Inu nokha Mbuyanga, Bwenzi ndi mtsogozi,
Ndikondetsa Inutu, Kuposa za dziko
4. Msangalatsi ndi Inu, M’dziko la ucimo,
Ndikuganizani’nu M’zipata za m’Mwamba.