Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #209

Hymn 209 Ntayenda Nanu

[V1]
Ngati a Kumwamba,
Ntaunikidwa panjira,
Yofitsa kwa Yesu

2. Mzimu Woyera bwerani,
Mtehnga wa mpumulo;
Ndidana nazo zoipa,
Zotilekanitsa

3. Ndinakondwa nthawi ija!
Sindingaiwaile,
Ndatsala m’zobvuta zokha,
Dziko ndi lacabe.

4. Fano ndinalikondalo,
Kaya ndi lotani,
Thangateni kulicotsa,
nditsale ndi Inu

209. Ntayenda Nanu

Link copied to clipboard successfully!