Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #207
Hymn 207 Cikhululukiro Coona
[V1]
SEALS MY PARDON 1. Ndinaona pa Mtandapo
Wothatha ndi mwazi
Ali kundiyang’anitsa,
Pafupi ndi mtanda
2. Sindihta Kuiwala,
Zomwe ndinaona
Ngati ndine ndinamupha,
Zidziwika zokha
3. Anandiyang’anitsanso,
Ngati kundiuza
Imfa yino, mwazi uno,
zikupulumutsa
4. Chimo langa linamupha,
Loda ngati mdima,
Cinsisi ca cisomoco,
Cakhululukira
SEALS MY PARDON 1. Ndinaona pa Mtandapo
Wothatha ndi mwazi
Ali kundiyang’anitsa,
Pafupi ndi mtanda
2. Sindihta Kuiwala,
Zomwe ndinaona
Ngati ndine ndinamupha,
Zidziwika zokha
3. Anandiyang’anitsanso,
Ngati kundiuza
Imfa yino, mwazi uno,
zikupulumutsa
4. Chimo langa linamupha,
Loda ngati mdima,
Cinsisi ca cisomoco,
Cakhululukira