Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #127

Hymn 127 Mulungu Asamalabe

[V1]
Mulungu asamalabe Mbalame zonsezo;
Ngatitu azikondadi, Akonda inenso.

[C]
Andikonda, andikonda, Akonda inenso;
Akonda zinthu zonsezo, Akonda inenso.

[V2]
Maluwa mthengo monsemo Apanga Mbuyeyo;
Ngatitu awakondadi, Akonda inenso.

[C]
Andikonda, andikonda, Akonda inenso;
Akonda zinthu zonsezo, Akonda inenso.

[V3]
Mulungu, mlengi wathuyo Apanga zonsezo;
Samaiwala ana ’ke, Akonda onsewo.

[C]
Andikonda, andikonda, Akonda inenso;
Akonda zinthu zonsezo, Akonda inenso.

127. Mulungu Asamalabe

Link copied to clipboard successfully!