Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #123
Hymn 123 Dzina Lopambana Mmwamba
[V1]
Dzina lopambana m’mwamba, Ndi pa dziko lonselo,
Lomwe ’Tate anamutcha Mwana wake mmodziyo.

[C]
Dzina loyeratu (loyera), Dzina lofatsanso (lofatsa),
Lomwe nalinena angelowo.
Pa usiku uja (dzinalo), Dzina lokomatu (dzinalo),
Ndilo la Ambuye Yesu.

[V2]
Dzinalo lipatsa dalo, Ndi chimwemwe mtimanga,
Ndidzauza anthu ena Za chokoma chakecho.

[V3]
Moyo wanga udzayimba Za chikondi chakecho;
Ndidzatamandabe dzina, Lopambana onsewo.