Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #101
Hymn 101 Yesu Alikuitana
[V1]
JESUS IS CALLING 1. Yesu alikuitana iwe, Lero lomwe, lero lomwe;
Bwanji unasocherera iwe, Kutali kutaliko?

[C]
Aitana lero lomwe; Yesu alikuitana iwe tsopano.
(Tenor and Bass):
Aitana lero lomwe; Aitana lero lomwe;
Yesu alikuitana lero, ’itana iwe tsopano.
2. Yesu aitana wotopa ’we, Lero lomwe, lero lomwe
Tula katundu wako pa Iye; Ndipo sadzakukana.
3. Yesu alikulindira iwe, Lero lomwe, lero lomwe;
Idza ndi machimo ako onse; Idzatu usachedwe.
4. Yesu ali kudandaulira, Lero lomwe, lero lomwe;
Okhulupira adzakondwera; Podzakomana naye.