Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #6
Hymn 6 Yesu Akudza
[V1]
WATCH YE SAINTS 1 Yang’anirani Akristu, Zammwamba zigwedezeka
Yatsani nyali zanuzo, Kukomana naye Mbuye.

[C]
Onani Yesu adza; Akudza mulemerero,
Adzakhala mfumu yathu, Onani! Ali kudza.
2 Ona lonjezano lace, Wakhululukira tchimo,
Mwazi nutsuka minjiro, Nena nthano ya chombolo.
3 Mafumu anjenjemera, Imva! ali kudza ndithu
Nena za cisomo chake, M’mene lipenga lilira.
4 Mitundu yonse idzatha, Khristu wafulumiratu;
Dziko lili kutha ndithu; Mbuye wathu ali kudza.
5 Yesu aitana nonse, Akupembedzera inu;
Kangaza nthawi ikutha, Ungadzatsaletu kunja.