Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #330
Hymn 330 Lemekeza Mlungu Tate
[V1]
GROLY BE TO GOD THE FATHER 1. Lemekeza Mlungu ’tate, Lemekeza Mwananso,
Lemekeza, Mlungu Mzimu, Mlungu Mmodzi mkuruyo;
Lemekeza, lemekeza, Mlungu wathu yemweyo.
2. Mlemekeze, anaconda, Natisuka m’mtimamo,
Anatiombola ife, Tikhale nayeyo;
Lemekeza, lemekeza, Yesu Mbuye nsembeyo.
3. Lemekeza Mfumu yathu, Mfumu, Mlengi wathuyo,
Apambana anthu onse, Pansi ndi kumwambako;
Lemekeza, lemekeza, Mfumu ya mafumuyo.