Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #328

Hymn 328 NATIONAL ATHEM (Chichewa)

[V1]
Mumsunge m’mtendere,
Khonjetsani adani onse,
Njala nthenda nsanje,
Lunzitsani mitima yathu,
Kuti tisaope,
Mdalitse mtsogoleri nafe,
Ndi Mayi Malawi,

2. Malawi dziko lokongola,
Lachonde ndi ufulu,
Nyanja ndi mphepo ya m’mapiri,
Ndithudi tadala,
Zigwa, mapiri, nthaka, Dzinthu
Mphatso zaulere
Nkhalango, madambo abwino
Ngokoma Malawi.

[V3]
O’ Ufulu tigwirizane,
Kukweza Malawi
Ndi chikondi, khama kumvera,
Timutumikire
Pa nkhondo nkana pa mtendere
Cholinga n’chimodzi
Mayi, Bambo, tidzipereke
Pokweza Malawi

328. NATIONAL ATHEM (Chichewa)

Link copied to clipboard successfully!