Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #326
Hymn 326 Mpingo Wa Akristu ’Fe
[V1]
WE’RE A LITTLE CHRISTIAN BAND 1. Mpingo wa Akristu ’fe, tikondwra mwa Ambuye
Tinka m’dziko labwino, tikondwera mwa Ambuye.

[C]
Mpulumutsi, Mtitsogoze bwino bwino,
Pakupita kunka mmwambamo.
2. Timayenda bwinotu, tikondwera mwa Ambuye
Tigonjetsa mdaniyo, tikondwera mwa Ambuye.
3. Msanga tidzapumadi, tikondwera mwa Ambuye
Tidzabvala kronayo, tikondwra mwa Ambuye.