Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #308
Hymn 308 Polenga Dzikoli
[V1]
LET THERE BE LIGHT 1. Polenga dzikoli, Pakumva Inudi, Kwayeratu;
Mumve pemperoli, Ndipo pamenepa, Palibe mauwo, Muwaletu.
2. Inu wakudzatu Kuwaciritsadi A nthendawo;
Kupatsa moyowo, Kuona m’masomo, pa anthu onsewo, Muwaletu.
3. Mzimu woonadi, Ndi wa cikondico, Idzanitu
Mwamba mulengemo, Pali za mdimazo, Pa dziko ponsepo, Muwaletu
4. Inu Atatuwo, Wodala Mlunguyo, Timveretu,
Malengedwewo, Mdima ukhalamo, Mutume mauwo Muwaletu