Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #304

Hymn 304 Atate Wa Kumwambako

[V1]
FATHER, SON, AND SPIRIT 1. Atate wa kumwambako, Munaombla ife ndi
Cikondi canu cijaco, Tiyamikira inutu.

2. Ambuye Yesu ndinutu, Munabadwira anthu ’fe
Munatifera tonse fe, Tiyamikira Inutu

3. Mzimu woyera m’timamo, Tiyeretsedwe ndinunso,
Munatisunga bwinoli, Tiyamikira Inutu.

4. Atate, Mwana, Mzimunso, Ndinu atatu mmodzitu,
Ocimwa tinipemphhako, Mutikhululukire ’fe.

304. Atate Wa Kumwambako

Link copied to clipboard successfully!